Surah Al-A'raf (The Heights ) - Aya 90

Surah Al-A'raf (The Heights ) - Chewa - Aya 90 Aya count 206

وَقَالَ ٱلْمَلَأُ ٱلَّذِينَ كَفَرُوا۟ مِن قَوْمِهِۦ لَئِنِ ٱتَّبَعْتُمْ شُعَيْبًا إِنَّكُمْ إِذًۭا لَّخَٰسِرُونَ ﴿٩٠﴾
Ndipo akuluakulu mwa anthu ake omwe sadakhulupirire adati: “Ngati mutsatira Shuaib ndithudi pamenepo ndiye kuti mukhala otayika.”
Share