Surah Al-Hashr ( The Gathering ) - Aya 21

Surah Al-Hashr ( The Gathering ) - Chewa - Aya 21 Aya count 24

لَوْ أَنزَلْنَا هَٰذَا ٱلْقُرْءَانَ عَلَىٰ جَبَلٍۢ لَّرَأَيْتَهُۥ خَٰشِعًۭا مُّتَصَدِّعًۭا مِّنْ خَشْيَةِ ٱللَّهِ ۚ وَتِلْكَ ٱلْأَمْثَٰلُ نَضْرِبُهَا لِلنَّاسِ لَعَلَّهُمْ يَتَفَكَّرُونَ ﴿٢١﴾
Chikhala kuti tidaivumbulutsa Qur’an iyi pamwamba pa phiri, ukadaliona phirilo lili lodzichepetsa ndi kung’ambika chifukwa choopa Allah. Ndipo awa ndi mafanizo omwe tikuwapereka kwa anthu kuti aganizire.
Share