Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Aya 95

Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Chewa - Aya 95 Aya count 111

قُل لَّوْ كَانَ فِى ٱلْأَرْضِ مَلَٰٓئِكَةٌۭ يَمْشُونَ مُطْمَئِنِّينَ لَنَزَّلْنَا عَلَيْهِم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ مَلَكًۭا رَّسُولًۭا ﴿٩٥﴾
Nena: “Padziko pakadakhala angelo omayendayenda ndi okhazikika (m’malo awo ndi m’nyumba zawo), tikadawatsitsira m’ngelo monga mtumiki kuchokera kumwamba.”
Share