Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Aya 90

Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Chewa - Aya 90 Aya count 111

وَقَالُوا۟ لَن نُّؤْمِنَ لَكَ حَتَّىٰ تَفْجُرَ لَنَا مِنَ ٱلْأَرْضِ يَنۢبُوعًا ﴿٩٠﴾
Ndipo (pamene adalephera kubwera ndi Qur’an yawo,) adati: “Sitingakukhulupirire mpaka utatitulutsira kasupe wosaphwa m’dziko (lathu ili la Makka).”
Share