Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Aya 61

Surah Al-Isra ( The Night Journey ) - Chewa - Aya 61 Aya count 111

وَإِذْ قُلْنَا لِلْمَلَٰٓئِكَةِ ٱسْجُدُوا۟ لِءَادَمَ فَسَجَدُوٓا۟ إِلَّآ إِبْلِيسَ قَالَ ءَأَسْجُدُ لِمَنْ خَلَقْتَ طِينًۭا ﴿٦١﴾
Ndipo (akumbutse) pamene tidauza angelo kuti: “Mugwadireni Adam.” Ndipo adamugwadira kupatula Iblis (iye) adati: “Kodi ndimugwadire yemwe mwamlenga ndi dongo?”
Share